1 Samueli 17:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Kenako Davide anathamanga nʼkukaima pambali pake. Atatero anasolola lupanga la Mfilisitiyo+ mʼchimake nʼkumudula mutu pofuna kutsimikizira kuti wafadi. Afilisiti ataona kuti ngwazi yawo yamphamvu ija yafa, anayamba kuthawa.+ 1 Samueli 17:54 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 54 Kenako Davide anatenga mutu wa Mfilisiti uja nʼkupita nawo ku Yerusalemu koma zida za Mfilisitiyo anaziika mutenti yake.+
51 Kenako Davide anathamanga nʼkukaima pambali pake. Atatero anasolola lupanga la Mfilisitiyo+ mʼchimake nʼkumudula mutu pofuna kutsimikizira kuti wafadi. Afilisiti ataona kuti ngwazi yawo yamphamvu ija yafa, anayamba kuthawa.+
54 Kenako Davide anatenga mutu wa Mfilisiti uja nʼkupita nawo ku Yerusalemu koma zida za Mfilisitiyo anaziika mutenti yake.+