Salimo 18:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Yehova amandidalitsa mogwirizana ndi chilungamo changa.+Amandipatsa mphoto chifukwa choti ndine wosalakwa.*+ Salimo 91:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mulungu ananena kuti: “Popeza amandikonda,* ine ndidzamupulumutsa.+ Ndidzamuteteza chifukwa akudziwa* dzina langa.+
20 Yehova amandidalitsa mogwirizana ndi chilungamo changa.+Amandipatsa mphoto chifukwa choti ndine wosalakwa.*+
14 Mulungu ananena kuti: “Popeza amandikonda,* ine ndidzamupulumutsa.+ Ndidzamuteteza chifukwa akudziwa* dzina langa.+