Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 2:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Choncho Solomo anachotsa Abiyatara kuti asatumikirenso monga wansembe wa Yehova ndipo izi zinakwaniritsa mawu amene Yehova analankhula ku Silo+ okhudza nyumba ya Eli.+

  • 1 Mafumu 2:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Zitatero, mfumu inasankha Benaya+ mwana wa Yehoyada kuti akhale mkulu wa asilikali mʼmalo mwa Yowabu, ndipo inasankha wansembe Zadoki+ kuti alowe mʼmalo mwa Abiyatara.

  • 1 Mbiri 29:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Pa tsikulo, iwo anadya ndi kumwa mosangalala kwambiri+ pamaso pa Yehova. Kachiwirinso, anaveka Solomo mwana wa Davide ufumu ndipo anamudzoza pamaso pa Yehova kukhala mtsogoleri.+ Anadzozanso Zadoki kukhala wansembe.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena