1 Samueli 31:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Nkhondo inamʼkulira kwambiri Sauli, moti oponya mivi ndi uta anamupeza nʼkumuvulaza koopsa.+ 1 Samueli 31:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho Sauli, ana ake atatu, womunyamulira zida komanso asilikali ake onse anafera limodzi pa tsikuli.+
6 Choncho Sauli, ana ake atatu, womunyamulira zida komanso asilikali ake onse anafera limodzi pa tsikuli.+