2 Samueli 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno Hiramu+ mfumu ya Turo anatumiza anthu kwa Davide. Anatumizanso matabwa a mkungudza,+ akalipentala komanso anthu oswa miyala yomangira makoma ndipo anayamba kumanga nyumba* ya Davide.+
11 Ndiyeno Hiramu+ mfumu ya Turo anatumiza anthu kwa Davide. Anatumizanso matabwa a mkungudza,+ akalipentala komanso anthu oswa miyala yomangira makoma ndipo anayamba kumanga nyumba* ya Davide.+