1 Samueli 28:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Afilisiti anasonkhana nʼkukamanga msasa ku Sunemu.+ Nayenso Sauli anasonkhanitsa Aisiraeli onse nʼkukamanga msasa ku Giliboa.+ 1 Mbiri 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Afilisiti anayamba kumenyana ndi Aisiraeli ndipo asilikali a Isiraeli ankathawa moti ambiri anaphedwa mʼphiri la Giliboa.+
4 Afilisiti anasonkhana nʼkukamanga msasa ku Sunemu.+ Nayenso Sauli anasonkhanitsa Aisiraeli onse nʼkukamanga msasa ku Giliboa.+
10 Afilisiti anayamba kumenyana ndi Aisiraeli ndipo asilikali a Isiraeli ankathawa moti ambiri anaphedwa mʼphiri la Giliboa.+