1 Mbiri 14:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Davide anadziwa kuti Yehova wachititsa kuti ufumu wake ukhazikike mu Isiraeli,+ popeza ufumu wakewo unakwezedwa kwambiri chifukwa cha anthu a Mulungu, Aisiraeli.+ 1 Mbiri 14:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Davide anatchuka mpaka mbiri yake inamveka kumayiko onse ndipo Yehova anachititsa kuti anthu a mitundu yonse azimuopa Davideyo.+
2 Davide anadziwa kuti Yehova wachititsa kuti ufumu wake ukhazikike mu Isiraeli,+ popeza ufumu wakewo unakwezedwa kwambiri chifukwa cha anthu a Mulungu, Aisiraeli.+
17 Davide anatchuka mpaka mbiri yake inamveka kumayiko onse ndipo Yehova anachititsa kuti anthu a mitundu yonse azimuopa Davideyo.+