24 Ndikulumbira mʼdzina la Yehova Mulungu wamoyo, amene anandiika pampando wachifumu wa Davide bambo anga komanso amene anachititsa kuti ufumu wanga ukhazikike+ ndiponso kuti pakhale mzere wa banja lachifumu+ mogwirizana ndi zimene analonjeza, lero Adoniya aphedwa.”+