1 Mbiri 28:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anandiuza kuti: ‘Mwana wako Solomo ndi amene adzamange nyumba yanga ndiponso mabwalo anga, chifukwa ndamusankha kuti akhale mwana wanga ndipo ine ndidzakhala bambo ake.+ Mateyu 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Panamvekanso mawu ochokera kumwamba+ onena kuti: “Uyu ndi Mwana wanga+ wokondedwa ndipo amandisangalatsa kwambiri.”+ Aheberi 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mwachitsanzo, kodi Mulungu anauzapo mngelo uti kuti: “Iwe ndiwe mwana wanga. Lero ine ndakhala bambo ako”?+ Komanso kuti: “Ine ndidzakhala bambo ake ndipo iye adzakhala mwana wanga”?+
6 Anandiuza kuti: ‘Mwana wako Solomo ndi amene adzamange nyumba yanga ndiponso mabwalo anga, chifukwa ndamusankha kuti akhale mwana wanga ndipo ine ndidzakhala bambo ake.+
17 Panamvekanso mawu ochokera kumwamba+ onena kuti: “Uyu ndi Mwana wanga+ wokondedwa ndipo amandisangalatsa kwambiri.”+
5 Mwachitsanzo, kodi Mulungu anauzapo mngelo uti kuti: “Iwe ndiwe mwana wanga. Lero ine ndakhala bambo ako”?+ Komanso kuti: “Ine ndidzakhala bambo ake ndipo iye adzakhala mwana wanga”?+