2 Samueli 23:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Awa ndi mayina a asilikali amphamvu a Davide:+ Yosebu-basebete mbadwa ya Hakemoni, mtsogoleri wa amuna atatu.+ Iye anatenga mkondo wake nʼkupha anthu 800 nthawi imodzi. 2 Samueli 23:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 ndi Uriya+ Muhiti, onse pamodzi analipo 37. 1 Mafumu 15:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Anatero popeza Davide anachita zoyenera pamaso pa Yehova, ndipo anatsatira chilichonse chimene Mulungu anamulamula masiku onse a moyo wake, kupatulapo pa nkhani ya Uriya Muhiti.+
8 Awa ndi mayina a asilikali amphamvu a Davide:+ Yosebu-basebete mbadwa ya Hakemoni, mtsogoleri wa amuna atatu.+ Iye anatenga mkondo wake nʼkupha anthu 800 nthawi imodzi.
5 Anatero popeza Davide anachita zoyenera pamaso pa Yehova, ndipo anatsatira chilichonse chimene Mulungu anamulamula masiku onse a moyo wake, kupatulapo pa nkhani ya Uriya Muhiti.+