1 Samueli 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iye anawauza kuti: “Munthu amene adzakhale mfumu yanuyo azidzachita izi:+ Azidzatenga ana anu+ kuti azikayenda mʼmagaleta ake+ ndiponso kukwera pamahatchi* ake.+ Ena mwa ana anuwo azidzathamanga patsogolo pa magaleta ake. 1 Mafumu 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pa nthawi imeneyi Adoniya+ mwana wa Hagiti anayamba kudzikweza nʼkumanena kuti: “Ineyo ndikhala mfumu!” Iye anapangitsa galeta ndipo anali ndi amuna okwera pamahatchi* komanso amuna 50 oti azithamanga patsogolo pake.+ Miyambo 11:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kudzikweza kukafika manyazi amafikanso,+Koma anthu odzichepetsa ndi amene ali ndi nzeru.+
11 Iye anawauza kuti: “Munthu amene adzakhale mfumu yanuyo azidzachita izi:+ Azidzatenga ana anu+ kuti azikayenda mʼmagaleta ake+ ndiponso kukwera pamahatchi* ake.+ Ena mwa ana anuwo azidzathamanga patsogolo pa magaleta ake.
5 Pa nthawi imeneyi Adoniya+ mwana wa Hagiti anayamba kudzikweza nʼkumanena kuti: “Ineyo ndikhala mfumu!” Iye anapangitsa galeta ndipo anali ndi amuna okwera pamahatchi* komanso amuna 50 oti azithamanga patsogolo pake.+