2 Samueli 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pa nthawiyi, Davide anabereka ana aamuna ku Heburoni.+ Mwana wake woyamba anali Aminoni+ ndipo mayi ake anali Ahinowamu+ wa ku Yezereeli.
2 Pa nthawiyi, Davide anabereka ana aamuna ku Heburoni.+ Mwana wake woyamba anali Aminoni+ ndipo mayi ake anali Ahinowamu+ wa ku Yezereeli.