-
2 Samueli 20:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Mfumu Davide atafika kunyumba yake* ku Yerusalemu,+ anatenga akazi ake aangʼono 10, amene anawasiya kuti azisamalira nyumba yake aja+ nʼkuwatsekera mʼnyumba ina ndipo anaikapo alonda. Iye ankawapatsa chakudya koma sanagone nawo.+ Iwo anapitiriza kukhala mʼnyumbamo mpaka tsiku limene anamwalira. Ankakhala ngati akazi amasiye ngakhale kuti mwamuna wawo anali moyo.
-