1 Samueli 27:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Sauli atamva kuti Davide wathawira ku Gati, anasiya kumusakasaka.+ 1 Mbiri 18:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Patapita nthawi, Davide anagonjetsa Afilisiti+ nʼkuwalanda mzinda wa Gati+ ndi midzi yake yozungulira.
18 Patapita nthawi, Davide anagonjetsa Afilisiti+ nʼkuwalanda mzinda wa Gati+ ndi midzi yake yozungulira.