1 Samueli 22:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma mwana mmodzi wamwamuna wa Ahimeleki, mwana wa Ahitubu, dzina lake Abiyatara+ anapulumuka ndipo anathawa nʼkutsatira Davide. 1 Samueli 30:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako Davide anauza Abiyatara+ wansembe, mwana wa Ahimeleki kuti: “Chonde bweretsa efodi.”+ Choncho Abiyatara anapititsa efodi kwa Davide.
20 Koma mwana mmodzi wamwamuna wa Ahimeleki, mwana wa Ahitubu, dzina lake Abiyatara+ anapulumuka ndipo anathawa nʼkutsatira Davide.
7 Kenako Davide anauza Abiyatara+ wansembe, mwana wa Ahimeleki kuti: “Chonde bweretsa efodi.”+ Choncho Abiyatara anapititsa efodi kwa Davide.