2 Samueli 15:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Iwo alinso ndi ana awo awiri komweko, Ahimazi+ mwana wa Zadoki ndi Yonatani+ mwana wa Abiyatara. Ndiye mukatume ana awowo kuti adzandiuze zonse zimene mungamve.” 2 Samueli 17:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndiye tumizani uthenga mwamsanga kwa Davide wakuti, ‘Usiku uno musakhale pamalo owolokera kuchipululu. Koma muwoloke ndithu chifukwa mukapanda kutero inu mfumu ndi anthu onse amene muli nawo, muphedwa.’”+ 2 Samueli 17:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Anthuwo atachoka, Ahimazi ndi Yonatani anatuluka mʼchitsimemo nʼkupita kukauza Mfumu Davide kuti: “Nyamukani mwamsanga ndipo muwoloke mtsinje.” Kenako anawauza malangizo amene Ahitofeli anapereka.+
36 Iwo alinso ndi ana awo awiri komweko, Ahimazi+ mwana wa Zadoki ndi Yonatani+ mwana wa Abiyatara. Ndiye mukatume ana awowo kuti adzandiuze zonse zimene mungamve.”
16 Ndiye tumizani uthenga mwamsanga kwa Davide wakuti, ‘Usiku uno musakhale pamalo owolokera kuchipululu. Koma muwoloke ndithu chifukwa mukapanda kutero inu mfumu ndi anthu onse amene muli nawo, muphedwa.’”+
21 Anthuwo atachoka, Ahimazi ndi Yonatani anatuluka mʼchitsimemo nʼkupita kukauza Mfumu Davide kuti: “Nyamukani mwamsanga ndipo muwoloke mtsinje.” Kenako anawauza malangizo amene Ahitofeli anapereka.+