Mateyu 21:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Atayandikira ku Yerusalemu nʼkufika ku Betefage paphiri la Maolivi, Yesu anatuma ophunzira awiri.+ Mateyu 24:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Atakhala pansi mʼphiri la Maolivi, ophunzira anabwera kwa iye ali payekha nʼkumufunsa kuti: “Tiuzeni, kodi zinthu zimenezi zidzachitika liti, ndipo chizindikiro cha kukhalapo* kwanu+ ndi cha mapeto a nthawi* ino+ chidzakhala chiyani?” Machitidwe 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kenako anabwerera ku Yerusalemu,+ kuchokera kuphiri la Maolivi. Phiri limeneli lili pafupi ndi Yerusalemu, pa mtunda wa ulendo wa tsiku la sabata.*
21 Atayandikira ku Yerusalemu nʼkufika ku Betefage paphiri la Maolivi, Yesu anatuma ophunzira awiri.+
3 Atakhala pansi mʼphiri la Maolivi, ophunzira anabwera kwa iye ali payekha nʼkumufunsa kuti: “Tiuzeni, kodi zinthu zimenezi zidzachitika liti, ndipo chizindikiro cha kukhalapo* kwanu+ ndi cha mapeto a nthawi* ino+ chidzakhala chiyani?”
12 Kenako anabwerera ku Yerusalemu,+ kuchokera kuphiri la Maolivi. Phiri limeneli lili pafupi ndi Yerusalemu, pa mtunda wa ulendo wa tsiku la sabata.*