1 Samueli 31:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Anthu a ku Yabesi-giliyadi+ atamva zimene Afilisiti anamuchita Sauli, 1 Samueli 31:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Atatero, anatenga mafupa awo+ nʼkuwaika mʼmanda pansi pa mtengo wa bwemba ku Yabesi+ ndipo anasala kudya masiku 7.
13 Atatero, anatenga mafupa awo+ nʼkuwaika mʼmanda pansi pa mtengo wa bwemba ku Yabesi+ ndipo anasala kudya masiku 7.