2 Mbiri 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Nayonso Mfumu Solomo inapatsa mfumukazi ya ku Sheba chilichonse chimene inkafuna komanso chimene inapempha. Inapatsa mfumukaziyo zoposa zimene inabweretsa. Kenako mfumukaziyo inanyamuka nʼkumapita kwawo limodzi ndi antchito ake.+
12 Nayonso Mfumu Solomo inapatsa mfumukazi ya ku Sheba chilichonse chimene inkafuna komanso chimene inapempha. Inapatsa mfumukaziyo zoposa zimene inabweretsa. Kenako mfumukaziyo inanyamuka nʼkumapita kwawo limodzi ndi antchito ake.+