Salimo 122:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndipo tsopano mapazi athu aimaPamageti ako iwe Yerusalemu.+ Salimo 122:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chifukwa kumeneko nʼkumene kunaikidwa mipando yachiweruzo,+Mipando yachifumu ya nyumba ya Davide.+