Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 49:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Yuda ndi mwana wa mkango.+ Mwana wanga, ukadzadya nyama imene wapha udzachokapo. Iye wapinda mawondo ake nʼkudziwongola ngati mkango umene wagona pansi. Ndipo mofanana ndi mkango, ndi ndani amene angamudzutse?

  • Numeri 23:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Uwu ndi mtundu wa anthu umene udzadzuka ngati mkango,

      Udzanyamuka ngati mkango.+

      Sudzagona pansi mpaka utadya nyama

      Ndi kumwa magazi a nyama zophedwazo.”

  • Numeri 24:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Iye wagwada pansi, wagona pansi ngati mkango,

      Ngati mkango, ndani angayese kumʼdzutsa?

      Amene akudalitsa iwe adzadalitsidwa,

      Ndipo amene akukutemberera, adzatembereredwa.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena