Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 1:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Solomo anasonkhanitsa magaleta ndi mahatchi,* moti anakhala ndi magaleta 1,400 ndi mahatchi* 12,000.+ Zonsezi ankazisunga mʼmizinda yosungiramo magaleta+ ndiponso pafupi ndi mfumuyo ku Yerusalemu.+

  • 2 Mbiri 9:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Solomo anali ndi makola 4,000 a mahatchi ndi magaleta komanso mahatchi* okwana 12,000.+ Zonsezi ankazisunga mʼmizinda yosungiramo magaleta ndiponso pafupi ndi mfumuyo ku Yerusalemu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena