2 Mbiri 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mfumuyo inachititsa kuti ku Yerusalemu siliva ndi golide akhale wambiri ngati miyala+ ndiponso kuti matabwa a mkungudza akhale ambiri ngati mitengo yamkuyu ya ku Sefela.+ 2 Mbiri 9:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Mfumuyo inachititsa kuti ku Yerusalemu kukhale siliva wambiri ngati miyala ndiponso kuti matabwa a mkungudza akhale ambiri ngati mitengo ya mkuyu ya ku Sefela.+
15 Mfumuyo inachititsa kuti ku Yerusalemu siliva ndi golide akhale wambiri ngati miyala+ ndiponso kuti matabwa a mkungudza akhale ambiri ngati mitengo yamkuyu ya ku Sefela.+
27 Mfumuyo inachititsa kuti ku Yerusalemu kukhale siliva wambiri ngati miyala ndiponso kuti matabwa a mkungudza akhale ambiri ngati mitengo ya mkuyu ya ku Sefela.+