-
2 Mbiri 1:16, 17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Mahatchi a Solomo ankawagula kuchokera ku Iguputo+ ndipo gulu la amalonda a mfumu linkagula mahatchiwo mʼmagulumagulu.*+ 17 Galeta lililonse lochokera ku Iguputo mtengo wake unali ndalama zasiliva 600 pomwe mtengo wa hatchi unali ndalama zasiliva 150. Ndipo iwo ankagulitsa zinthuzi kwa mafumu onse a Ahiti ndi mafumu a ku Siriya.
-