Yoswa 22:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Zitatero, anthu a fuko la Rubeni, la Gadi ndi hafu ya fuko la Manase, anachoka ku Silo kumene kunali Aisiraeli mʼdziko la Kanani. Anabwerera ku Giliyadi,+ kudera limene Mose anawapatsa molamulidwa ndi Yehova kuti azikhalako.+
9 Zitatero, anthu a fuko la Rubeni, la Gadi ndi hafu ya fuko la Manase, anachoka ku Silo kumene kunali Aisiraeli mʼdziko la Kanani. Anabwerera ku Giliyadi,+ kudera limene Mose anawapatsa molamulidwa ndi Yehova kuti azikhalako.+