1 Mafumu 18:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno Ahabu anauza Obadiya kuti: “Pita mʼdzikoli, ukayendere akasupe onse a madzi ndi zigwa* zonse. Mwina tikhoza kupeza udzu wobiriwira woti tizidyetsa mahatchi ndi nyulu,* kuti ziweto zathuzi zisafe zonse.”
5 Ndiyeno Ahabu anauza Obadiya kuti: “Pita mʼdzikoli, ukayendere akasupe onse a madzi ndi zigwa* zonse. Mwina tikhoza kupeza udzu wobiriwira woti tizidyetsa mahatchi ndi nyulu,* kuti ziweto zathuzi zisafe zonse.”