2 Mafumu 4:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndiyeno mayiyo anatenga mwanayo nʼkukamugoneka pabedi la munthu wa Mulungu woona uja.+ Atatero anatuluka nʼkutseka chitseko. 2 Mafumu 4:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Elisa atalowa mʼnyumbamo, anapeza mwana wakufayo atamʼgoneka pabedi lake lija.+
21 Ndiyeno mayiyo anatenga mwanayo nʼkukamugoneka pabedi la munthu wa Mulungu woona uja.+ Atatero anatuluka nʼkutseka chitseko.