Salimo 99:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mose ndi Aroni anali mʼgulu la ansembe ake,+Ndipo Samueli anali mʼgulu la anthu amene ankaitana pa dzina lake.+ Iwo ankaitana Yehova,Ndipo iye ankawayankha.+
6 Mose ndi Aroni anali mʼgulu la ansembe ake,+Ndipo Samueli anali mʼgulu la anthu amene ankaitana pa dzina lake.+ Iwo ankaitana Yehova,Ndipo iye ankawayankha.+