1 Mafumu 17:2, 3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako Eliya anamva mawu a Yehova akuti: 3 “Uchoke kuno nʼkulowera chakumʼmawa ndipo ukabisale mʼchigwa* cha Keriti chimene chili kumʼmawa kwa Yorodano.
2 Kenako Eliya anamva mawu a Yehova akuti: 3 “Uchoke kuno nʼkulowera chakumʼmawa ndipo ukabisale mʼchigwa* cha Keriti chimene chili kumʼmawa kwa Yorodano.