Yoswa 19:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Alameleki, Amadi ndi Misali. Analowera kumadzulo nʼkukafika ku Karimeli+ ndi ku Sihori-libanati. Yoswa 19:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ichi chinali cholowa cha fuko la Aseri motsatira mabanja awo+ ndipo imeneyi inali mizinda yawo ndi midzi yake.
31 Ichi chinali cholowa cha fuko la Aseri motsatira mabanja awo+ ndipo imeneyi inali mizinda yawo ndi midzi yake.