Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 44:19, 20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Palibe amene amaganiza mumtima mwake

      Kapena amene akudziwa zinthu, kapenanso amene amamvetsa zinthu kuti adzifunse kuti:

      “Hafu ya mtengowu ndasonkhera moto,

      Ndipo pamakala ake ndaphikapo mkate komanso ndawotcha nyama nʼkudya.

      Ndiye kodi wotsalawu ndipangire chinthu chonyansa?+

      Kodi zoona ndilambire chinthu chopangidwa ndi mtengo?”*

      20 Iye akudya phulusa.

      Mtima wake umene wapusitsidwa wamusocheretsa.

      Iye sangathe kudzipulumutsa kapena kunena kuti:

      “Kodi chinthu chimene chili mʼdzanja langa lamanjachi si chabodza?”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena