17 Eliya anali munthu ngati ife tomwe, komabe atapemphera kuchokera pansi pamtima kuti mvula isagwe, mvula sinagwedi mʼdzikolo kwa zaka zitatu ndi miyezi 6.+ 18 Kenako anapempheranso ndipo mvula inagwa kuchokera kumwamba moti nthaka inatulutsa zipatso zake.+