Yoswa 19:17, 18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Maere a 4+ anagwera Isakara,+ kapena kuti ana a Isakara motsatira mabanja awo. 18 Malire a gawo lawo anakafika ku Yezereeli,+ Kesulotu, Sunemu,+ 1 Mafumu 21:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kenako panachitika nkhani yokhudza munda wa mpesa wa Naboti wa ku Yezereeli. Mundawu unali ku Yezereeli,+ pafupi ndi nyumba yachifumu ya Ahabu mfumu ya Samariya.
17 Maere a 4+ anagwera Isakara,+ kapena kuti ana a Isakara motsatira mabanja awo. 18 Malire a gawo lawo anakafika ku Yezereeli,+ Kesulotu, Sunemu,+
21 Kenako panachitika nkhani yokhudza munda wa mpesa wa Naboti wa ku Yezereeli. Mundawu unali ku Yezereeli,+ pafupi ndi nyumba yachifumu ya Ahabu mfumu ya Samariya.