1 Mafumu 16:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ngati kuti kuyenda mʼmachimo a Yerobowamu+ mwana wa Nebati kunali kosakwanira, Ahabu anakwatira Yezebeli+ mwana wa Etibaala mfumu ya Asidoni,+ ndipo anayamba kutumikira Baala+ nʼkumamugwadira.
31 Ngati kuti kuyenda mʼmachimo a Yerobowamu+ mwana wa Nebati kunali kosakwanira, Ahabu anakwatira Yezebeli+ mwana wa Etibaala mfumu ya Asidoni,+ ndipo anayamba kutumikira Baala+ nʼkumamugwadira.