Ekisodo 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kenako Farao anamva za nkhaniyi ndipo ankafuna kupha Mose. Koma Mose anathawa Farao nʼkupita kukakhala kudziko la Midiyani.+ Atafika kumeneko, anakhala pafupi ndi chitsime. 1 Samueli 27:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma Davide anaganiza kuti: “Tsiku lina Sauli adzandipha ndithu. Chanzeru chimene ndingachite nʼkuthawira+ kudziko la Afilisiti. Ndiyeno Sauli adzasiya kundifunafuna mʼdziko lonse la Isiraeli+ ndipo ndidzapulumuka mʼmanja mwake.”
15 Kenako Farao anamva za nkhaniyi ndipo ankafuna kupha Mose. Koma Mose anathawa Farao nʼkupita kukakhala kudziko la Midiyani.+ Atafika kumeneko, anakhala pafupi ndi chitsime.
27 Koma Davide anaganiza kuti: “Tsiku lina Sauli adzandipha ndithu. Chanzeru chimene ndingachite nʼkuthawira+ kudziko la Afilisiti. Ndiyeno Sauli adzasiya kundifunafuna mʼdziko lonse la Isiraeli+ ndipo ndidzapulumuka mʼmanja mwake.”