-
1 Mafumu 19:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Yezebeli atamva zimenezo, anatuma munthu kwa Eliya kukamuuza kuti: “Milungu yanga indilange mowirikiza, ngati pofika nthawi ino mawa sindidzakhala nditakupha ngati mmene waphera aneneriwo.”
-
-
Aroma 11:2, 3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Mulungu sanakane anthu ake amene anali oyambirira kuwavomereza.+ Kodi simukudziwa zimene lemba lina limanena zokhudza Eliya, pamene anachonderera Mulungu motsutsa Aisiraeli? Limati: 3 “Yehova,* iwo apha aneneri anu ndipo agwetsa maguwa anu ansembe moti ine ndatsala ndekhandekha. Tsopano ayambanso kundifunafuna kuti andiphe.”+
-