Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 14:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Zitatero, asilikali onse amene anali pamalowo komanso amene anali kutchire mumsasa anayamba kuchita mantha. Nawonso asilikali amene ankalanda katundu+ anayamba kuchita mantha. Nthaka inayamba kugwedezeka ndipo Mulungu anachititsa kuti Afilisiti achite mantha.

  • Yobu 9:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Amagwedeza dziko lapansi nʼkulisuntha pamalo ake,

      Moti zipilala zake zimagwedera.+

  • Salimo 68:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Dziko lapansi linagwedezeka,+

      Kumwamba kunagwa mvula chifukwa cha inu Mulungu,

      Phiri la Sinai ili linagwedezeka chifukwa cha inu Mulungu, Mulungu wa Isiraeli.+

  • Nahumu 1:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Mapiri akuluakulu amagwedezeka chifukwa cha iye.

      Ndipo mapiri angʼonoangʼono amasungunuka.+

      Dziko lapansi lidzanjenjemera chifukwa cha nkhope yake

      Pamodzi ndi nthaka komanso zinthu zonse zokhala mʼdzikomo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena