-
2 Mafumu 8:7, 8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Kenako Elisa anapita ku Damasiko+ ndipo pa nthawiyo nʼkuti Beni-hadadi+ mfumu ya Siriya akudwala. Choncho mfumuyo inauzidwa kuti: “Munthu wa Mulungu woona+ uja wabwera kuno.” 8 Mfumuyo itamva zimenezi, inauza Hazaeli+ kuti: “Tenga mphatso ndipo upite kwa munthu wa Mulungu woonayo.+ Ukafunse kwa Yehova kudzera mwa iye kuti, ‘Kodi ndichira matenda angawa?’”
-