-
2 Mafumu 2:23, 24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Kenako Elisa ananyamuka nʼkumapita ku Beteli. Ali mʼnjira, anyamata ena a mumzindawo anayamba kumunyoza+ kuti: “Choka kuno wadazi iwe! Choka kuno wadazi iwe!” 24 Kenako Elisa anatembenuka nʼkuwayangʼana ndipo anawatemberera mʼdzina la Yehova. Ndiyeno zimbalangondo+ ziwiri zazikazi zinatuluka patchire nʼkukhadzula anyamata 42.+
-