-
2 Mafumu 2:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Kenako ana a aneneri amene anali ku Yeriko anapita kwa Elisa nʼkumufunsa kuti: “Kodi ukudziwa kuti lero Yehova atenga mbuye wako kuti asakhalenso mtsogoleri wako?” Iye anayankha kuti: “Ndikudziwa zimenezo. Khalani chete.”
-