-
1 Mafumu 20:34Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
34 Beni-hadadi anauza Ahabu kuti: “Ndibweza mizinda imene bambo anga analanda bambo anu ndipo mukhoza kukhazikitsa misika* ku Damasiko ngati mmene bambo anga anachitira ku Samariya.”
Ahabu anayankha kuti: “Tikapanga pangano loti zikhaladi chonchi, ndikusiya kuti uzipita kwanu.”
Atatero anachita naye pangano ndipo anamusiya kuti azipita.
-