Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 2:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Pamene ankayenda, uku akulankhulana, anangoona galeta* lankhondo lowala ngati moto ndi mahatchi* owala ngati moto.+ Galeta ndi mahatchiwo zinadutsa pakati pawo nʼkuwalekanitsa ndipo Eliya anatengedwa mumphepo yamkuntho nʼkupita kumwamba.*+

  • Salimo 68:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Magaleta ankhondo a Mulungu ali mʼmagulu a masauzande osawerengeka, ali mʼmagulu masauzandemasauzande.+

      Yehova walowa mʼmalo oyera kuchokera kuphiri la Sinai.+

  • Zekariya 6:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Kenako nditayangʼananso kumwamba ndinaona magaleta 4 akubwera kuchokera pakati pa mapiri awiri. Mapiriwo anali akopa.*

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena