Genesis 4:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Adamu anagonanso ndi mkazi wake Hava ndipo anabereka mwana wamwamuna. Hava anapatsa mwanayo dzina lakuti Seti*+ chifukwa atabadwa, Havayo ananena kuti: “Mulungu wandipatsa* mwana wina mʼmalo mwa Abele amene Kaini anamupha.”+
25 Adamu anagonanso ndi mkazi wake Hava ndipo anabereka mwana wamwamuna. Hava anapatsa mwanayo dzina lakuti Seti*+ chifukwa atabadwa, Havayo ananena kuti: “Mulungu wandipatsa* mwana wina mʼmalo mwa Abele amene Kaini anamupha.”+