Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 1:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Pa nthawi imeneyi Adoniya+ mwana wa Hagiti anayamba kudzikweza nʼkumanena kuti: “Ineyo ndikhala mfumu!” Iye anapangitsa galeta ndipo anali ndi amuna okwera pamahatchi* komanso amuna 50 oti azithamanga patsogolo pake.+

  • 1 Mafumu 1:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Kenako Natani+ anauza Bati-seba+ mayi ake a Solomo+ kuti: “Kodi mwamva zoti Adoniya,+ mwana wa Hagiti, wakhala mfumu koma mbuye wathu Davide sakudziwa chilichonse?

  • 1 Mafumu 2:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Ndikulumbira mʼdzina la Yehova Mulungu wamoyo, amene anandiika pampando wachifumu wa Davide bambo anga komanso amene anachititsa kuti ufumu wanga ukhazikike+ ndiponso kuti pakhale mzere wa banja lachifumu+ mogwirizana ndi zimene analonjeza, lero Adoniya aphedwa.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena