2 Samueli 13:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Abisalomu mwana wa Davide, anali ndi mchemwali wake wokongola dzina lake Tamara.+ Ndipo mwana wina wa Davide, dzina lake Aminoni,+ anayamba kukonda kwambiri Tamara.
13 Abisalomu mwana wa Davide, anali ndi mchemwali wake wokongola dzina lake Tamara.+ Ndipo mwana wina wa Davide, dzina lake Aminoni,+ anayamba kukonda kwambiri Tamara.