Genesis 36:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho Esau anakakhazikika kudera lamapiri ku Seiri.+ Dzina lina la Esau linali Edomu.+