Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 66:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Ndidzaika chizindikiro pakati pawo ndipo ena mwa anthu amene adzapulumuke ndidzawatumiza ku mitundu ya anthu. Ndidzawatumiza kwa anthu aluso lokoka uta omwe ndi a ku Tarisi,+ ku Puli ndi ku Ludi.+ Ndidzawatumizanso kwa anthu a ku Tubala ndi ku Yavani+ komanso akuzilumba zakutali amene sanamvepo zokhudza ine kapena kuona ulemerero wanga. Iwo adzalengeza za ulemerero wanga pakati pa mitundu ya anthu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena