28 Ndidzapitiriza kumusonyeza chikondi changa chokhulupirika mpaka kalekale,+
Ndipo pangano limene ndinachita naye silidzaphwanyidwa.+
29 Ndidzachititsa kuti mbadwa zake zidzakhalepo kwamuyaya,
Ndipo ndidzachititsa kuti mpando wake wachifumu udzakhalepo mpaka kalekale ngati kumwamba.+