1 Mafumu 6:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Solomo anakuta mkati mwa nyumba yonseyo ndi golide woyenga bwino.+ Kutsogolo kwa chipinda chamkati+ anaikako matcheni agolide ndipo anakuta chipindacho ndi golide.
21 Solomo anakuta mkati mwa nyumba yonseyo ndi golide woyenga bwino.+ Kutsogolo kwa chipinda chamkati+ anaikako matcheni agolide ndipo anakuta chipindacho ndi golide.