1 Mbiri 24:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Davide, komanso Zadoki+ yemwe anali wochokera mwa ana a Eleazara, ndiponso Ahimeleki wochokera mwa ana a Itamara, anagawa ana a Aroniwo mʼmagulu mogwirizana ndi udindo wa utumiki wawo.
3 Davide, komanso Zadoki+ yemwe anali wochokera mwa ana a Eleazara, ndiponso Ahimeleki wochokera mwa ana a Itamara, anagawa ana a Aroniwo mʼmagulu mogwirizana ndi udindo wa utumiki wawo.